Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 17:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mwamuna wosadulidwa, wosadulidwa khungu lace munthuyo amsadze mwa anthu a mtundu wace; waphwanya pangano langa.

Werengani mutu wathunthu Genesis 17

Onani Genesis 17:14 nkhani