Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 13:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Dziko lonse siliri pamaso pako kodi? Ulekanetu ndi ine: ukanka iwe ku dzanja lamanzere, ine ndinka ku dzanja lamanja: ukanka iwe ku dzanja lamanja, ine ndinka ku dzanja lamanzere.

Werengani mutu wathunthu Genesis 13

Onani Genesis 13:9 nkhani