Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 13:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Loti anatukula maso ace nayang'ana cigwa conse ca Yordano kuti conseco cinali ndi madzi ambiri, asanaononge Yehova Sodomu ndi Gomora, monga munda wa Yehova, monga dziko la Aigupto pakunka ku Zoari.

Werengani mutu wathunthu Genesis 13

Onani Genesis 13:10 nkhani