Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 1:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mulungu anapanga zinyama za dziko lapansi monga mwa mitundu yao; ndi ng'ombe monga mwa mtundu wace, ndi zonse zakukwawa pansi monga mwa mitundu yao; ndipo Mulungu anaona kuti kunali kwabwino.

Werengani mutu wathunthu Genesis 1

Onani Genesis 1:25 nkhani