Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 1:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo adati Mulungu, Dziko lapansi libale zamoyo monga mwa mitundu yao, ng'ombe, ndi zokwawa, ndi zinyama za dziko lapansi monga mwa mitundu yao: ndipo kunatero.

Werengani mutu wathunthu Genesis 1

Onani Genesis 1:24 nkhani