Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 5:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace atero Ambuye Yehova, Popeza kupokosera kwanu kwaposa kwa amitundu akukuzingani, ndipo simunayenda m'malemba anga, kapena kucita maweruzo anga, ngakhale maweruzo a amitundu akukuzingani simunawacita;

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 5

Onani Ezekieli 5:7 nkhani