Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 45:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kutengako malo opatulika akhale nayo mikono mazana asanu m'litali mwace, ndi mazana asanu kupingasa kwace, lamphwamphwa pozungulira pace; ndi pabwalo pace poyera pozungulira pace mikono makumi asanu.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 45

Onani Ezekieli 45:2 nkhani