Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 45:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pogawa dziko likhale calowa cao, mupereke copereka kwa Yehova, ndico gawo lopatulika la dziko; m'litali mwace likhale la mabango zikwi makumi awiri mphambu zisanu, ndi kupingasa kwace zikwi makumi awiri; likhale lopatulika m'malire ace onse pozungulira pace.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 45

Onani Ezekieli 45:1 nkhani