Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 45:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kuyambira poyesedwapo uyese zikwi makumi awiri mphambu zili sanu m'litali mwace, ndi zikwi khumi kupingasa kwace; m'menemo ndimo mukhale malo opatulika, ndiwo opatulika, ndiwo opatulikitsa.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 45

Onani Ezekieli 45:3 nkhani