Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 44:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akaturukira ku bwalo lakunja, ku bwalo lakunja kuti anthu, azibvula zobvala zao zimene atumikira nazo, naziike m'zipinda zopatulika, nabvale zobvala zina; angapatule anthu ndi zovala zao.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 44

Onani Ezekieli 44:19 nkhani