Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 43:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo miyeso ya guwa la nsembe, kuyesa mikono ndi iyi: (mkonowo ndiwo mkono ndi cikhato), tsinde lace likhale mkono, ndi kupingasa kwace mkono, ndi mkuzi wace m'mphepete mwace pozungulira pace kuyesa zala; ili ndi tsinde la guwali.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 43

Onani Ezekieli 43:13 nkhani