Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 43:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi kuyambira kunsi kwace kunthaka, kufikira phaka lamunsi, mikono iwiri; ndi kupingasa kwace mkono umodzi; ndi kuyambira phaka laling'ono kufikira phaka lalikuru mikono inai; ndi kupingasa kwace mkono.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 43

Onani Ezekieli 43:14 nkhani