Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 43:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Wabadwa ndi munthu iwe, onetsa nyumba ya Israyeli kacisiyu, kuti acite manyazi ndi mphulupulu zao; ndipo ayese muyeso wace.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 43

Onani Ezekieli 43:10 nkhani