Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 43:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ngati akacita manyazi nazo zonse anazicita, uwadziwitse maonekedwe a kacisiyu, ndi muyeso wace, ndi poturukira pace, ndi polowera pace, ndi malongosoledwe ace onse, ndi malemba ace onse, ngakhale maonekedwe ace onse, ndi malamulo ace onse; nuwalembere pamaso pao, kuti asunge maonekedwe ace onse, ndi malemba ace onse, nawacite.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 43

Onani Ezekieli 43:11 nkhani