Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 37:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati kwa ine, Nenera kwa mpweya, nenera, wobadwa ndi munthu iwe, nuti kwa mpweya, Atero Ambuye Yehova, Idza, mpweya iwe, kucokera ku mphepo zinai, nuuzire ophedwa awa, kuti akhale ndi moyo.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 37

Onani Ezekieli 37:9 nkhani