Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 37:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

M'mwemo ndinanenera monga anandiuza, ndi mpweya unawalowa, ndipo anakhala ndi moyo, naimirira ciriri, gulu la nkhondo lalikurukuru ndithu.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 37

Onani Ezekieli 37:10 nkhani