Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 26:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi ziboda za akavalo ace iye adzapondaponda m'makwalala ako onse; adzapha anthu ako ndi lupanga; ndi zoimiritsa za mphamvu yako zidzagwa pansi.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 26

Onani Ezekieli 26:11 nkhani