Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 26:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Papeza acuruka akavalo ace, pfumbi lao lidzakukuta; malinga ako adzagwedezeka ndi phokoso la apakavalo, ndi njinga za magareta, palowa iye pa zipata zako, monga umo amalowera m'mudzi popasukira linga lace.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 26

Onani Ezekieli 26:10 nkhani