Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 23:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzakuikira nsanje yanga, nadzakucitira mwaukali, iwowa adzakudula mphuno ndi makutu; ndi otsiriza ako adzagwa ndi lupanga, adzakucotsera ana ako amuna ndi akazi, ndi otsirizira ako adzatha ndi moto.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 23

Onani Ezekieli 23:25 nkhani