Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 12:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinacita monga momwe anandilamulira, ndinaturutsa akatundu anga usana, ngati a pa ulendo wa kundende, ndi madzulo ndinaboola pakhoma ndi dzanja langa, ndinawaturutsa pali mdima, ndi kuwasenza paphewa panga pamaso: pao.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 12

Onani Ezekieli 12:7 nkhani