Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezara 9:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsopano, kamphindi, Yehova Mulungu wathu wationetsa cisomo, kutisiyira cipulumutso, ndi kutipatsa ciciri m'malo mwace mopatulika; kuti Mulungu wathu atipenyetse m'maso mwathu, ndi kutitsitsimutsa pang'ono m'ukapolo wathu.

Werengani mutu wathunthu Ezara 9

Onani Ezara 9:8 nkhani