Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezara 9:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo ndinati, Mulungu wanga, ndigwa nkhope, ndi kucita manyazi kuweramutsa nkhope yanga kwa inu Mulungu wanga, popeza mphulupulu zathu zacuruka pamtu pathu, ndi kuparamula kwathu kwakula kufikira m'Mwamba.

Werengani mutu wathunthu Ezara 9

Onani Ezara 9:6 nkhani