Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezara 9:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi pa nsembe yamadzulo ndinanyamuka m'kuzunzika kwanga, cobvala canga ndi maraya anga zong'ambika; ndipo ndinagwada ndi maondo anga, ndi kutambasula manja anga kwa Yehova Mulungu wanga;

Werengani mutu wathunthu Ezara 9

Onani Ezara 9:5 nkhani