Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezara 9:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

amene munalamulira mwa atumiki anu aneneri ndi kuti, Dzikolo mumukako likhale colowa canu ndilo dziko lodetsedwa mwa cidetso ca anthu a m'maikomo, mwa zonyansa zao zimene zinalidzaza, kuyambira nsonga yina kufikira nsonga inzace ndi ucisi wao.

Werengani mutu wathunthu Ezara 9

Onani Ezara 9:11 nkhani