Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezara 9:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Zitatha izi tsono anandiyandikira akalonga, ndi kuti, Anthu a Israyeli, ndi ansembe, ndi Alevi, sanadzilekanitsa ndi anthu a maikowa, kunena za zonyansa zao za Akanani, Ahiti, Aperizi, Ayebusi, Aamoni, Amoabu, Aaigupto, ndi Aamori.

Werengani mutu wathunthu Ezara 9

Onani Ezara 9:1 nkhani