Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezara 10:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ayang'anire ici tsono akalonga athu a msonkhano wonse, ndi onse a m'midzi mwathu amene anadzitengera akazi acilendo abwere pa nthawi zoikika, ndi pamodzi nao akuru a mudzi wao uli wonse, ndi oweruza ace, mpaka udzaticokera mkwiyo waukali wa Mulungu wathu cifukwa ca mlandu uwu.

Werengani mutu wathunthu Ezara 10

Onani Ezara 10:14 nkhani