Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezara 10:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma anthu ndiwo ambiri, ndi nyengo yino nja mvula, tiribenso mphamvu yakuima pabwalo, ndi nchitoyi sindiyo ya tsiku limodzi kapena awiri; pakuti tacurukitsa kulakwa kwathu pa cinthu ici.

Werengani mutu wathunthu Ezara 10

Onani Ezara 10:13 nkhani