Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Estere 2:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, atamveka mau a mfumu ndi lamulo lace, ndipo atasonkhanidwa anamwali ambiri m'cinyumba ca ku Susani, awasunge Hege, anamtenga Estere yemwe, alowe m'nyumba ya mfumu, amsunge Hege wosunga akazi.

Werengani mutu wathunthu Estere 2

Onani Estere 2:8 nkhani