Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Estere 2:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo namwaliyo anamkomera, namcitira cifundo; ndipo anafulumira kumpatsa zace zomyeretsa, ndi magawo ace, ndi anamwali asanu ndi awiri oyenera kumpatsa ocokera m'nyumba ya mfumu; ndipo anamsuntha iye ndi anamwali ace akhale m'malo okometsetsa m'nyumba ya akazi.

Werengani mutu wathunthu Estere 2

Onani Estere 2:9 nkhani