Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Estere 1:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Inde tsiku lomwelo akazi akuru a Perisiya ndi Mediya, atamva macitidwe a mkazi wamkuruyo, adzatero nao momwemo kwa akalonga onse a mfumu. Ndi cipeputso ndi mkwiyo zidzacuruka.

Werengani mutu wathunthu Estere 1

Onani Estere 1:18 nkhani