Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Estere 1:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti macitidwe awa a mkazi wamkuruyo adzabuka kufikira akazi onse, kupeputsa amuna ao pamaso pao; anthu akati, Mfumu Ahaswero anati abwere naye Vasiti mkazi wamkuru pamaso pace, koma sanadza iye.

Werengani mutu wathunthu Estere 1

Onani Estere 1:17 nkhani