Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 8:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anacita comweco; pakuti Aroni anasamula dzanja lace ndi ndodo yace, napanda pfumbi lapansi, ndipo panali nsabwe pa anthu ndi pa zoweta; pfumbi lonse lapansi liinasanduka nsabwe m'dziko lonse la Aigupto.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 8

Onani Eksodo 8:17 nkhani