Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 8:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Alembi anateronso ndi matsenga ao kuonetsa nsabwe, koma sanakhoza; ndipo panali nsabwe pa anthu, ndi pa zoweta.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 8

Onani Eksodo 8:18 nkhani