Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 4:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Mose anatenga mkazi wace ndi ana ace amuna, nawakweza pa buru, nabwerera kumka ku dziko la Aigupto; ndipo Mose anagwira ndodo ya Mulungu m'dzanja lace.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 4

Onani Eksodo 4:20 nkhani