Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 4:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova ananena ndi Mose m'Midyani, Muka, bwerera kumka ku Aigupto; pakuti adafa anthu onse amene anafuna moyo wako.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 4

Onani Eksodo 4:19 nkhani