Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 4:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose anabwera namuka kwa Yetero mpongozi wace, nanena naye, Ndimuketu, ndibwerere kumka kwa abale anga amene ali m'Aigupto, ndikaone ngati akali ndi moyo. Ndipo Yetero ananena ndi Mose, Pita bwino.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 4

Onani Eksodo 4:18 nkhani