Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 39:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo anaomba zobvala zakutumikira nazo ndi lamadzi, ndi lofiirira, ndi lofiira, atumikire nazo m'malo opatulika, naomba zobvala zopatulika za Aroni; monga Yehova adamuuza Mose.

2. Ndipo anaomba efodi wa golidi, lamadzi, lofiirira, ndi lofiira, ndi bafuta wa thonje losansitsa.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 39