Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 39:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anasula golidi waphanthiphanthi, nalemba nsambo, kuti amuombe pamodzi ndi lamadzi, ndi lofiirira, ndi lofiira, ndi bafuta wa thonje losansitsa, nchito ya mmisiri.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 39

Onani Eksodo 39:3 nkhani