Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 39:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anaomba zobvala zakutumikira nazo ndi lamadzi, ndi lofiirira, ndi lofiira, atumikire nazo m'malo opatulika, naomba zobvala zopatulika za Aroni; monga Yehova adamuuza Mose.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 39

Onani Eksodo 39:1 nkhani