Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 38:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo siliva wa iwo owerengedwa a khamulo ndiwo matalente zana limodzi, ndi masekeli cikwi cimodzi, kudza mazana asanu ndi awiri, mphambu makumi asanu ndi awiri kudza asanu, kuyesa sekeli wa malo opatulika;

Werengani mutu wathunthu Eksodo 38

Onani Eksodo 38:25 nkhani