Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 38:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Golidi yense anacita naye mu nchito yonse ya malo opatulika, golidi wa coperekaco, ndico matalente makumi awiri kudza asanu ndi anai, ndi masekeli mazana asanu ndi awiri, kudza makumi atatu, monga mwa sekeli wa malo opatulika.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 38

Onani Eksodo 38:24 nkhani