Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 38:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

munthu mmodzi anapereka beka, ndiwo limodzi la magawo awiri la sekeli, kuyesa sekeli wa malo opatulika, anatero onse akupita kumka kwa owerengedwawo, kuyambira munthu wa zaka makumi awiri ndi oposa, ndiwo anthu zikwi mazana asanu ndi limodzi kudza zitatu, ndi mazana asanu mphambu makumi asanu.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 38

Onani Eksodo 38:26 nkhani