Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 26:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo uzipanga kacisi ndi nsaru zophimba khumi, za bafuta wa thonje losansitsa, ndi thonje lamadzi, ndi lofiirira, ndi lofiira; uombemo akerubi, nchito ya mmisiri.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 26

Onani Eksodo 26:1 nkhani