Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 26:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Utali wace wa nsaru yophimba imodzi ndiwo mikono makumi awiri kudza isanu ndi itatu, ndi kupingasa kwa nsaru imodzi ndiko mikono inai; nsaru zonse zikhale za muyeso umodzi.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 26

Onani Eksodo 26:2 nkhani