Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 2:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamene anakabvundukula, anapenya mwanayo; ndipo, taonani, khandalo lirikulira. Ndipo anamva naye cifundo, nati, Uyu ndiye wa ana a Ahebri.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 2

Onani Eksodo 2:6 nkhani