Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 2:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo mlongo wace ananena ndi mwana wamkazi wa Farao, Ndipite ine kodi kukuitanirani woyamwitsa wa Ahebri, akuyamwitsireni mwanayo?

Werengani mutu wathunthu Eksodo 2

Onani Eksodo 2:7 nkhani