Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 7:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo adzakukondani, ndi kukudalitsani, ndi kukucurukitsani; adzadalitsanso zipatso za thupi lanu, ndi zipatso za nthaka yanu, tirigu wanu, ndi vinyo wanu, ndi mafuta anu, zoswana za ng'ombe zanu, ndi ana a nkhosa anu, m'dziko limene analumbirira makolo anu kuti adzakupatsani.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 7

Onani Deuteronomo 7:13 nkhani