Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 7:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kudzakhala, cifukwa ca kumvera inu maweruzo awa, ndi kuwasunga, ndi kuwacita, Yehova Mulungu wanu adzakusungirani cipangano ndi cifundo cimene analumbirira makolo anu;

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 7

Onani Deuteronomo 7:12 nkhani