Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 31:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti nditakalowetsa awa m'dziko limene ndinalumbirira makolo ao, moyenda mkaka ndi uci ngati madzi; ndipo atadya nakhuta, nanenepa, pamenepo adzatembenukira milungu yina, ndi kuitumikira, ndi kundipeputsa Ine, ndi kutyola cipangano canga.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 31

Onani Deuteronomo 31:20 nkhani