Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 3:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kufikira Yehova atapumulitsa abale anu, monga anapumulitsa inu, nalandira iwonso dziko limene Yehova Mulungu wanu awapatsa tsidya lila la Yordano; pamenepo mudzabwerera munthu yense ku colowa cace, cimene ndinakupatsani.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 3

Onani Deuteronomo 3:20 nkhani